
Buku Lophunzitsila magulu a kumudzi download here
Bukuli lapangidwa ndi cholinga chofuna kuthandiza magulu a kumidzi kuti athe kukwanitsa maudindo ndi ntchito zawo potero athe kukhala magulu omwe angathe kuonetsetsa kuti boma likuwathandiza mokwanira kuchita zinthu mosabisa komanso mopanda chinyengo kuchokera kwa anthu ogwira ntchito za boma ndi atsogoleri

Amayi pa Chisankho download here
bungwe la Pan African Civic Educators Network (PACENET) likufuna kupereka bukhu limeneli kwa amayi omwe akufuna kukhala makhansala kapena aphungu kuti aligwiritse ntchito ngati chipangizo choti chiwathandize kudziwa zinthu zofunika zomwe zingawapangitse kukhala anthu aphindu

Governance Handbook download here
The Pan African Civic Educators Network (PACENET) seeks to work with local governance structures,namely,Village Development Committees (VDCs) and Area Development Committees (ADCs) to build their capacity to understand their functions, roles and responsibilities

A Trainer's Handbook for Community based structures download here
This handbook is designed to empower community based structures so that they are able to fulfil their roles and responsibilities including oversight functions hence ensuring that there is a critical pool of local communities that are able to demand for better social service delivery, transparency and accountability from duty bearers and power holders

Liu Lathu Newsletter download here
This is PACENET's 2012 Newsletter.
Have a Story to Share?
PACENET is always looking for newsworthy stories and ideas for publication